Mawa Em Kay Kadulo ali ndi uthenga Kwa ex wake komaso Kwa ex wanu mu fan rated performance yake.
Paja Ife za anthu okuti anaoneranapo sitimalowerera nde timva zambiri mu Fan Rated performance yake.
komaso osaiwala nyamata wa AI , Q_Pester komaso Kay Brein kuti Fan Rated anaipasa kale moto🔥. Linkie👇
1
237
Producer WACHIKAZI uja Ngelo waitulutsa yake.
Ngelo ft Em El & Lil Al akuti Gwengwe, khalidwe lawo lija ma SLIME ndekuti kulifotokoza Itaako ndi Ibeeere mwachilendo.
Zambiri mkanema wawoyi ku YouTube
5
267
PRINCE LUV AKUWOTCHA!
Video ya nyimbo yake ya Over yafika pa ma views 300K mu masiku atatu okha! Chikondi cha mafani chikuoneka ndipo ma number akulankhula okha. Pa liwiro limeneli, 1 million views si patali. Prince Luv akuphika moto!
64
Tineneso zoyenera kuchita apa? Kapena mwazimva kale fungo ndalama kuti nthawi yakwana yokha. Apa ali live ndipo chuma chigawidwaso. Komabe enanu ma village people akufuna mukhalebe osauka ndipk akugwesani mphwayi kuti musapange nawo izi.
1
134
Apa zalowa pokomera a Business ku Civo Stadium. Ghetto, kungosonkherana pachi gang gang nkugula stall imodzi ya Bar, mukhala kuti za January mwapanga
60
MISS MALAWI 2027
Apa aliyese akuona kuti zinthu zayamba, ndipo mwayi ndiwa aliyese amene ali ndi zomuyenereza. Nthawi ndiyomweyi, osati muzayambe kutokota zinthu zitafika kumapeto. Kwanuko amene mukumuona kuti ndi oyenera kutenga nawo gawo pa chinthuchi, Muwuzeni makomo atsekulidwa ndithu apa ayese mwayi wake.
Ipangeni Tag Ngengeyo komaso iwonetseni ka link aka ( missmw.org ) kapena phone number iyi (0996109177)kuti itsate bwinobwino momwe zikuyendera zinthuzi.
53
Pena pake akufuna mkazi okongola wa mbuyo komanso shape yabwino otha kuyankhula bwino both English and Chichewa akapange advert. Fee is K1 million everything. Kutchukaso pompo.
Contact Akometsi via WhatsApp: 0892821969
Note: We have used Temwah’s photo to give you an idea of what they are looking for. Ngati sukufika ma level awa chonde osatiyatsana nthawi data ikudula.
"Mwati degree mukuyifanizila ndi ndalama ? ndinu opusa zedi" Small Wife walankhulako choncho !
2
499
Koditu ANAWA sakubwera moyesa, ndipo sakugona tulo kapena kukhutira ndi zochepa zomwe anapeza. Shano Index akupitiliza kuika moto maka pa nkhani yoimilira ana ama 2pin. Ndiye akuti mawa chikutulutsaso ina.
2
325
Dreezy Hussle akumuchonderera girlfriend wake kuti akumbukire malonjezo amene anamupanga mu nyimbo yake ya Kumbuka. Bro, akukumbukira zonse! Koma vuto ndilakuti bank balance ya mwamuna wina yalemba kale chapter yatsopano ya chikondi chawo!
1
328
Uyu ndi Nayomi, amayika komanso amaphunzitsa anthu kupanga ma nails ndima eye rashes. A girlfriend anu aja akaphunzire kwa uyu asiye kuwoneka ngati gule. Zala ngati satana munthu wapa banja 🙌🏽
WhatsApp her akuphunzitse: 0990388625
Ma live akupitilira ndipo panopa walowaso live. Omwe anapanga join dzulo atha kuperekera umboni ngati wa Maranatha chifukwa kwaperekedwa 1 Million grand prize.
Ngati simunayambe kutsatira, pangani izi
1. Click link ( kick.com/rayhan265 )
2. Open account
3. Follow him
Kwinako keep joining the live streams link yake yomweyo ndipo mukatelo ma points anu azichuluka mpaka muzikhala ndi mwayi owina ma change.
Mwana wake ndi emwe uja ali pa Khameli.
784
Up and coming artists from Mangochi and Domasi omwe akufuna kukapanga perform ku ma show awa a GWAMBA, contact this guy
+265899333532 (WhatsApp only and no calls)
Anthu 5 okha oyambilira basi.
Kodi ku Kasunguko mukuti waiswera mtima sosobina iyi ndi ndan?, kumeneko mukuchulusa chibwana, Akometsi mupezereni kamnyamata koti kakamuziziritse mtima Nestar Nyamachika chifukwa amuchita chija ndi chipongwe.
2
702





















