iam_Karonga 🇲🇼🥷 retweeted
PLEASE LET'S HELP CATHERINE WITH ANY LITTLE AMOUNT THAT WE HAVE.🙏
Dzina langa ndi Catherine Kawerere, ndili ndi zaka 22, ndimakhala ku Kasungu.
Kuyambira 2019 ndili ndi vuto la impsyo (kidneys). Tsopano madokotala akuti ndikufunika Kidney Transplant ku India mwachangu.
Wopereka Kidney wapezeka kale, koma ndikufunika *K46 Million* kuti ulendowu utheke. Makolo anga alibe kuthekera.
Sabata iliyonse ndimafunika ndipita ku Kamuzu Central Hospital kawiri ku Dialysis.
Chonde ndithandizeni, ngakhale kugawana uthengawu.
Kulumikizana:
0995759754 - Catherine
0999635902 - Masauko Kawerere
0996761010 / 0999641497 - Getrude Nthukwa
Bank:
Standard Bank: 10003020336
Acc Name: Masauko Kawerere
RT for awareness.🙏❤️
Ipite ku Blantyre
Illusionz has temporarily closed from today as it prepares to relocate to a new venue in Lilongwe’s CBD. 👀
The move follows Sogecoa Limited’s decision to convert part of the Golden Peacock Complex, originally intended for entertainment and nightclub operations, into residential facilities.
456
iam_Karonga 🇲🇼🥷 retweeted
Happy birthday baby Naylah 🥹❤️🎂 ONE whole year of you my baby!!!The sweetest, happiest, easiest little person to love. 🥹 You are truly God’s gift to us, and watching you grow has been the most beautiful blessing. We love you beyond words 🎀❤️
iam_Karonga 🇲🇼🥷 retweeted
Lets talk. Message the number for enquiry.
Please repost, someone on your TL maybe looking for help.






























