Gadabwali retweeted
If you ever see me doing some stupid don’t blame my parents. Those guys did their best. Okanika ndife chabe.
Gadabwali retweeted
Anyone who claims that their political party does no wrong and the other party does no right is either a liar, a fool or both.
Gadabwali retweeted
Malawi. Dziko losaka. Kusaka mafuta. Kusaka forex. Kusaka network. Kusaka chilungamo. Kusaka ntchito. Kusaka mbewa. Kusaka chilichonse. Ndikamaliza kenako ndisakenso mkazi. – at Malawi
Gadabwali retweeted
Osamabisa madalitso anu kuti Mulungu azilandila ulemelero wake. I’m calling this one VENOM ⚫️ (Kapena kuti “Ululu”). – at Malawi
Gadabwali retweeted
Aise ngati achina Madalitso sizikuwayendera ndiye kuli bwanji achina Mavuto, Ziwone ndi Pililani
Gadabwali retweeted
Every morning you’re supposed to smoke. That’s why they call it M’mbanda kucha 🤷🏾♂️
































